Dataset Viewer (First 5GB)
audio
audioduration (s) 4.8
18.5
| raw_text
stringlengths 49
236
| normalized_text
stringlengths 52
267
| gender
stringclasses 16
values |
---|---|---|---|
Mtsogoleri wa mpingo wa Seventh Day m'chigawo cha pakati a John Phiri ati ndi kofunika kuti mpingo udzikhala ndi atolankhani kuti azithandizira kufikitsa patali uthenga wabwino | Mtsogoleri wa mpingo wa sevenifi deyi m'chigawo cha pakati a Joni Phiri ati ndi kofunika kuti mpingo udzikhala ndi atolankhani kuti azithandizira kufikitsa patali uthenga wabwino | female |
|
A Phiri anena izi pamene amatseka mwambo wophunzitsa atolankhani a mpingowu omwe udachitikira pa sukulu ya Nalikule ku Lilongwe kwa masiku atatu | A Phiri anena izi pamene amatseka mwambo wophunzitsa atolankhani a mpingowu omwe udachitikira pa sukulu ya Nalikule ku Lilongwe kwa masiku atatu | female |
|
A Phiri ati, atolankhani a m'dziko sangakwanitse kulemba chilichonse kotero ndi bwino kuphunzitsa atolankhani a mumpingo | A Phiri ati, atolankhani a m'dziko sangakwanitse kulemba chilichonse kotero ndi bwino kuphunzitsa atolankhani a mumpingo | female |
|
kuti azithandizira kulemba nkhani zomwe zikuchitika m'mipingo mwawo, komanso kufikitsa uthenga wachipulumutso patali | kuti azithandizira kulemba nkhani zomwe zikuchitika m'mipingo mwawo, komanso kufikitsa uthenga wachipulumutso patali | female |
|
Mkhalakale pa nyimbo za uzimu Bertha Nkhoma lero adasangalatsa odwala komanso odikilira odwalawa ndi uthenga wachiyembekezo pa chipatala chachikulu m'boma la Salima, ndi nyimbo yake yatsopano yotchedwa Chipambano | Mkhalakale pa nyimbo za uzimu Befa Nkhoma lero adasangalatsa odwala komanso odikilira odwalawa ndi uthenga wachiyembekezo pa chipatala chachikulu m'boma la Salima, ndi nyimbo yake yatsopano yotchedwa Chipambano | female |
|
A Nkhoma ati nyimboyi ikukamba zonena kuti ngakhale mavuto akule bwanji koma Chipambano chimabwera pamapeto pake kotero anthu asamataye mtima pa chilichonse | A Nkhoma ati nyimboyi ikukamba zonena kuti ngakhale mavuto akule bwanji koma Chipambano chimabwera pamapeto pake kotero anthu asamataye mtima pa chilichonse | female |
|
Izi zachitika pamapeto a ntchito zokonza komanso kupereka katundu wosiyanasiyana kwa odwala pachipatala chachikulu m'boma la Salima | Izi zachitika pamapeto a ntchito zokonza komanso kupereka katundu wosiyanasiyana kwa odwala pachipatala chachikulu m'boma la Salima | female |
|
Nduna yoona za ulimi, a Sam Kawale, yati unduna wawo umakhulupilira kuti njala, umphawi komanso kusowa kwa ndalama, zikhoza kutha alimi m'dziko muno atayamba kuchita ulimi ngati malonda | Nduna yoona za ulimi, a Sam Kawale, yati unduna wawo umakhulupilira kuti njala, umphawi komanso kusowa kwa ndalama, zikhoza kutha alimi m'dziko muno atayamba kuchita ulimi ngati malonda | female |
|
A Kawale anena izi lero pamene amayendera minda ya anthu amene apindula ndi ngongole ya bungwe la boma lobwerketsa ndalama la National Economic Empowerment Fund,Neef m'dera la mfumu yaikulu Santhe, m'boma la Kasungu | A Kawale anena izi lero pamene amayendera minda ya anthu amene apindula ndi ngongole ya bungwe la boma lobwerketsa ndalama la Neshono ikonomiki impawamenti Fandi , Nifi m'dera la mfumu yaikulu Santhe, m'boma la Kasungu | female |
|
Mwa zina, iwo ati kuti izi zitheke alimi m'dziko muno akuyenera kuyambapo kugwiritsa ntchito makina osati makasu ,ulimi wakasintha sintha komanso kuchita ulimi wa mthilira | Mwa zina, iwo ati kuti izi zitheke alimi m'dziko muno akuyenera kuyambapo kugwiritsa ntchito makina osati makasu ,ulimi wakasintha sintha komanso kuchita ulimi wa mthilira | female |
|
Ndi chifukwa chake unduna wa za chuma kudzera ku bungwe la NEEF wayika ngongole yapadera imene ikuthandizira boma kuti alimi atukuke kufika poutenga ulimi kukhala bizinesi | Ndi chifukwa chake unduna wa za chuma kudzera ku bungwe la Nifi wayika ngongole yapadera imene ikuthandizira boma kuti alimi atukuke kufika poutenga ulimi kukhala bizinesi | female |
|
Komanso kukwaniritsa masomphenya a Malawi 2063," atero a Kawale | Komanso kukwaniritsa masomphenya a Malawi twente sikisite filii," atero a Kawale | female |
|
Mkulu wa NEEF, a Humphreys Mdyetseni, wati pofuna kukwaniritsa masomphenyawa, bungwe lawo liyamba kupereka ngongole yapadera ya ulimi wa mthilira kuyambira mwezi wa April chaka chino | Mkulu wa Nifi, a Hamfulezi Mdyetseni, wati pofuna kukwaniritsa masomphenyawa, bungwe lawo liyamba kupereka ngongole yapadera ya ulimi wa mthilira kuyambira mwezi wa Epulo chaka chino | female |
|
Ophunzira 58 a pa sukulu ya ukachenjede ya Mubas amene anali mamembala a DPP Youth Wing alengeza kuti atuluka m'chipani cha Democratic Progressive (DPP) | Ophunzira fifite eiti a pa sukulu ya ukachenjede ya Mubasi amene anali mamembala a Dipipi yufi wing’i alengeza kuti atuluka m'chipani cha demokilatiki pulogilesivi (Dipipi) | female |
|
M'modzi wa ophunzirawa, John Matipwiri wati iwo achita izi malinga ndi kuchotsedwa m'chipani kwa phungu wa dera la pakati m'boma la Mulanje, a Kondwani Nankhumwa | M'modzi wa ophunzirawa, John Matipwiri wati iwo achita izi malinga ndi kuchotsedwa m'chipani kwa phungu wa dera la pakati m'boma la Mulanje, a Kondwani Nankhumwa | female |
|
Iwo ati ndi okhumudwa ndi m'mene atsogoleri ena a chipani cha DPP akuyendetsera chipanichi, ndipo iwo ati atsatira a Nankhumwa, powalondola pa chiganizo chilichonse chimene apange | Iwo ati ndi okhumudwa ndi m'mene atsogoleri ena a chipani cha Dipipi akuyendetsera chipanichi, ndipo iwo ati atsatira a Nankhumwa, powalondola pa chiganizo chilichonse chimene apange | female |
|
Ophunzirawa anapezerapo danga pogwiritsa ntchito mwambo wa Social Weekend pofuna kupereka uthenga wawo | Ophunzirawa anapezerapo danga pogwiritsa ntchito mwambo wa sosho wikendi pofuna kupereka uthenga wawo | ||
Bungwe loona za ufulu wa anthu la Malawi Human Rights Commission lapempha apolisi kuti afufuze malipoti oti anthu ena akuopseza mtolankhani wa PIJ a Gregory Gondwe | Bungwe loona za ufulu wa anthu la Malawi yhumani laitsi komishoni lapempha apolisi kuti afufuze malipoti oti anthu ena akuopseza mtolankhani wa Piayijeyi a Giligole Gondwe | female |
|
komanso a Mercy Matonga a Times Group kutsatira nkhani zomwe adalemba kuti boma likuchitabe malonda ndi a Zuneth Sattar omwe akuwaganizira milandu ya katangale | komanso a Mese Matonga a taimusi gulupu kutsatira nkhani zomwe adalemba kuti boma likuchitabe malonda ndi a zunefi sata omwe akuwaganizira milandu ya katangale | female |
|
Malingana ndi chikalata chomwe wasainira ndi wapampando wa MHRC a Chikondi Chijozi, atolankhani komanso nyumba zofalitsa nkhani | Malingana ndi chikalata chomwe wasainira ndi wapampando wa Emu etchi alasi a Chikondi Chijozi, atolankhani komanso nyumba zofalitsa nkhani | female |
|
ali ndi ufulu wolemba nkhani mosaloweleredwa ndi boma ngakhale aliyense malingana ndi gawo 36 la malamulo oyendetsera dziko lino | ali ndi ufulu wolemba nkhani mosaloweleredwa ndi boma ngakhale aliyense malingana ndi gawo fetesikisi la malamulo oyendetsera dziko lino | female |
|
MHRC yati atolankhani alinso ndi udindo woonesetsa kuti adindo akulondolozedwa komanso kubweretsa pa mbalambanda zomwe zili zolakwika malingana ndi mfundo za demokalase | Emu etchi alasi yati atolankhani alinso ndi udindo woonesetsa kuti adindo akulondolozedwa komanso kubweretsa pa mbalambanda zomwe zili zolakwika malingana ndi mfundo za demokalase | female |
|
Mkulu wa asilikali a Paul Valentino Phiri komanso mlangizi wa boma pa malamulo a Thabo Chakaka Nyirenda | Mkulu wa asilikali a Poo Valentino Phiri komanso mlangizi wa boma pa malamulo a Thabo Chakaka Nyirenda | female |
|
adatsimikizira bungwe lomenyela ufulu atolankhani la Misa Malawi kuti atolankhaniwa asakhale mwa mantha ponena kuti sakufuna kuwamanga komanso saopsezedwa | adatsimikizira bungwe lomenyela ufulu atolankhani la Misa Malawi kuti atolankhaniwa asakhale mwa mantha ponena kuti sakufuna kuwamanga komanso saopsezedwa | female |
|
Nzika ya dziko lino yomwe imakhaka m'dziko la South Africa a Sando Jackson yapempha Amalawi omwe amakhala m'maiko ena kuti azikumbuka kumudzi | Nzika ya dziko lino yomwe imakhaka m'dziko la saufi afilika a Sando Jakisoni yapempha Amalawi omwe amakhala m'maiko ena kuti azikumbuka kumudzi | female |
|
ndi thandizo losiyanasiyana pa nthawi ino pamene dziko la Malawi lakhudzidwa ndi njala | ndi thandizo losiyanasiyana pa nthawi ino pamene dziko la Malawi lakhudzidwa ndi njala | female |
|
A Sando auza Times 360 Malawi kuti ntchito yothandiza anthu ndi ya aliyense amene ali ndi kuthekera kothandiza nzika za dziko lake | A Sando auza Taimusi fili sikisite Malawi kuti ntchito yothandiza anthu ndi ya aliyense amene ali ndi kuthekera kothandiza nzika za dziko lake | female |
|
Iwo alakhula izi pamene amagawa thandizo la ufa wa ndalama zokwana K320,000 kwa mabanja okwana 50 m'mudzi wa mfumu yaikulu Amidu m'boma la Balaka | Iwo alakhula izi pamene amagawa thandizo la ufa wa ndalama zokwana fili handede andi tuwente sauzande kwa mabanja okwana fifite m'mudzi wa mfumu yaikulu Amidu m'boma la Balaka | female |
|
M'modzi wa anthu amene alandira thandizoli Aisha Chibwana wayamikira kamba ka thandizoli potengera njala yomwe yakhudza bomali | M'modzi wa anthu amene alandira thandizoli Aisha Chibwana wayamikira kamba ka thandizoli potengera njala yomwe yakhudza bomali | female |
|
Anyamata oyimba magitala afika ndithu ku tchalitchi cha Flood mu mzinda wa Blantyre komwe akufuna kuba nawo nzeru kumbali yoimba gitala mozama kuchokera kwa katswiri woyimba Erik Paliani | Anyamata oyimba magitala afika ndithu ku tchalitchi cha Fuladi mu mzinda wa Bulantaya komwe akufuna kuba nawo nzeru kumbali yoimba gitala mozama kuchokera kwa katswiri woyimba Eliki Paliyani | female |
|
Nkhani yake ndi yoti chida ngati gitala nchofukira kwambiri mu maimbidwe | Nkhani yake ndi yoti chida ngati gitala nchofukira kwambiri mu maimbidwe | female |
|
Banja la a Kayiye ku chilomoni mu Mzinda wa Blantyre likuyembekezeka kuona kusitha pamene alandila thandizo la ufa, ndiwo komanso sopo mwa zina kuchokera ku gulu la Chilomoni girls | Banja la a Kayiye ku chilomoni mu Mzinda wa Bulantaya likuyembekezeka kuona kusitha pamene alandila thandizo la ufa, ndiwo komanso sopo mwa zina kuchokera ku gulu la Chilomoni gelozi | female |
|
A Elube Kayiye, omwe ali ndi ana khumi ndi m'modzi ndipo awiri mwa iwo ndi a ulumali ati thandizoli lafika munthawi yake pamene akhala akukumana ndi mavuto a chakudya | A Elube Kayiye, omwe ali ndi ana khumi ndi m'modzi ndipo awiri mwa iwo ndi a ulumali ati thandizoli lafika munthawi yake pamene akhala akukumana ndi mavuto a chakudya | female |
|
Group village headman Chibwana ati mabvuto oterewa ndi ochuluka kwambiri m'mudzi mwawo ndipo apempha akufuna kwabwino kuti azitha kuthandizapo | Gulupu vileji hedi mani Chibwana ati mabvuto oterewa ndi ochuluka kwambiri m'mudzi mwawo ndipo apempha akufuna kwabwino kuti azitha kuthandizapo | female |
|
Gulu la chilomoni girls linakayenderanso banja la a Nkumba lomwe abambo anyumbamo akhala akudwala nthenda yakufa ziwalo kwa zaka zisanu ndi zinayi tsopano | Gulu la chilomoni gelozi linakayenderanso banja la a Nkumba lomwe abambo anyumbamo akhala akudwala nthenda yakufa ziwalo kwa zaka zisanu ndi zinayi tsopano | female |
|
Anthu ena osadziwika adula ma polo a magets usiku wa Lachisanu mu Mzinda wa Mzuzu. Izi zachititsa kuti magetsi akhale ozima m'madera a New Katoto, Mchengautuwa, Area 4 ndi ena | Anthu ena osadziwika adula ma polo a magets usiku wa Lachisanu mu Mzinda wa Mzuzu. Izi zachititsa kuti magetsi akhale ozima m'madera a Nyu Katoto, Mchengautuwa, Areliya foloea 4 ndi ena | female |
|
Woyankhulira kampani ya Escom a Kitty Chingota wati mchitidwewu ndi wokhumudwitsa | Woyankhulira kampani ya Esikomu a Kite Chingota wati mchitidwewu ndi wokhumudwitsa | female |
|
Zeze Kingston naye anali nawo ku phwando lokumbukila kuti mkhalakale mu nkhani zotukula maimbidwe Jai Banda, 'Mr Entertainer' wakwanitsa zaka 65 Ku Mibawa mu mzinda wa Blantyre | Zeze King’isitoni naye anali nawo ku phwando lokumbukila kuti mkhalakale mu nkhani zotukula maimbidwe Jai Banda, 'Misita intatena' wakwanitsa zaka sikisite Ku Mibawa mu mzinda wa Bulantaya | female |
|
Iye anabwera atavala thalauza la jeans komanso uniform ya timu ya mpira ya Arsenal. Koma izi zinasephana ndi mabvalidwe a tsiku limenelo womwe anali zobvala zakuda komanso zoyera | Iye anabwera atavala thalauza la jinzi komanso unifomu ya timu ya mpira ya Aseno. Koma izi zinasephana ndi mavalidwe a tsiku limenelo womwe anali zobvala zakuda komanso zoyera | female |
|
Anthony Makondetsa akuti anthu ambiri chikondi chinatha kalekale m'makomo ndipo akungokhala, poti anazolowerana, mu nyimbo yake ija yoti Sudzampeza | Anthone Makondetsa akuti anthu ambiri chikondi chinatha kalekale m'makomo ndipo akungokhala, poti anazolowerana, mu nyimbo yake ija yoti Sudzampeza | female |
|
Mkhale kale pa nkhani zotukula luso, maka la maimbidwe Jai Banda, yemwe amadziwika kuti Mr Entertainer ali ndi chimwemwe chozaza tsaya chifukwa wakwanitsa zaka 65 | Mkhale kale pa nkhani zotukula luso, maka la maimbidwe Jai Banda, yemwe amadziwika kuti Misita Intatena ali ndi chimwemwe chozaza tsaya chifukwa wakwanitsa zaka sikisite faifi | female |
|
Pokondwerera chimenechi, a Classic Events anakonza chiphwando kukondwerera zaka 65 zakubadwa za Mr Entertainer ku Mibawa mu mzinda wa Blantyre | Pokondwerera chimenechi, a kilasiki iventsi anakonza chiphwando kukondwerera zaka sikisite faifi zakubadwa za Misita Intatena ku Mibawa mu mzinda wa Bulantaya | female |
|
Ku phwandoli kunabwera anthu ambiri ndipo kunalinso maimbidwe ochokera kwa oyimba osiyanasiyana monga Gibo Pearson komanso Zeze Kingston | Ku phwandoli kunabwera anthu ambiri ndipo kunalinso maimbidwe ochokera kwa oyimba osiyanasiyana monga Gibo Piyasoni komanso Zeze King’isitoni | female |
|
Ochita malonda pa msika wa Liwonde tsopano agwirizana ndi ganizo la khonsolo ya boma la Machinga yowasamutsira mkati mwa msikawu | Ochita malonda pa msika wa Liwonde tsopano agwirizana ndi ganizo la khonsolo ya boma la Machinga yowasamutsira mkati mwa msikawu | female |
|
Izi zadza kutsatira mkumano omwe unalipo lero Lachisanu pakati pa akuluakulu a khonsoloyi komanso ochita malondawa | Izi zadza kutsatira mkumano omwe unalipo lero Lachisanu pakati pa akuluakulu a khonsoloyi komanso ochita malondawa | female |
|
Wapampando wa komiti ya ochita malonda mu msikawu Samson Maleka wati ochita malondawa avomereza kuti asamukira mu msikawu mawa Loweruka | Wapampando wa komiti ya ochita malonda mu msikawu Samusoni Maleka wati ochita malondawa avomereza kuti asamukira mu msikawu mawa Loweruka | female |
|
pomwe khonsoloyi yalonjeza kuti ikonza mavuto omwe iwo akhala akuwadandaula | pomwe khonsoloyi yalonjeza kuti ikonza mavuto omwe iwo akhala akuwadandaula | female |
|
Lachinayi, anthu ochita malondawa anachita zionetsero, ati poonetsa kusakondwa ndi ganizo lowasamutsira mkati mwa msikawu | Lachinayi, anthu ochita malondawa anachita zionetsero, ati poonetsa kusakondwa ndi ganizo lowasamutsira mkati mwa msikawu | female |
|
ponena kuti khonsoloyi siimakonza ena mwa mavuto omwe analipo mu msikawu. Ndipo wapampando wa friends of Machinga a Smile Winess wapempha anthu a m'bomali | ponena kuti khonsoloyi siimakonza ena mwa mavuto omwe analipo mu msikawu. Ndipo wapampando wa fulenzi ofu Machinga a Simailo winesi wapempha anthu a m'bomali | female |
|
kuti azitha kutsata njira zoyenera zoperekera madandaulo awo m'malo mothamangira kuyambitsa mpungwepungwe omwe umaononga zambiri | kuti azitha kutsata njira zoyenera zoperekera madandaulo awo m'malo mothamangira kuyambitsa mpungwepungwe omwe umaononga zambiri | female |
|
Ochita malondawa akhala akunyanyala kudula ziphaso za malonda kwa zaka pafupifupi zisanu ndi zitatu 8 zomwe DC wabomali Rodrick Mateauma wati zimachititsa khonsoloyi kutolera ndalama zochepa. | Ochita malondawa akhala akunyanyala kudula ziphaso za malonda kwa zaka pafupifupi zisanu ndi zitatu eyiti zomwe Disii wabomali Rodiliki Mateauma wati zimachititsa khonsoloyi kutolera ndalama zochepa | female |
|
Anthu ena ochokera ku dera la pakati m'boma la Mulanje alengeza kuti atuluka m'chipani cha Democratic Progressive (DPP) | Anthu ena ochokera ku dera la pakati m'boma la Mulanje alengeza kuti atuluka m'chipani cha demokilatiki pulogilesivi (Dipipii) | female |
|
Anthuwa motsogozedwa ndi gavanala wa derali a Smart Ngalande, alengeza izi pa malo a Chisitu m'bomali | Anthuwa motsogozedwa ndi gavanala wa derali a Simati Ngalande, alengeza izi pa malo a Chisitu m'bomali | female |
|
Iwo ati achita izi malinga ndi kuchotsedwa m'chipani kwa phungu wa derali a Kondwani Nankhumwa | Iwo ati achita izi malinga ndi kuchotsedwa m'chipani kwa phungu wa derali a Kondwani Nankhumwa | female |
|
Pali mpungwepungwe pakati pa anthu ochita malonda a chimanga pa msika wa Mangochi turn off m'boma la Balaka | Pali mpungwepungwe pakati pa anthu ochita malonda a chimanga pa msika wa Mangochi theni ofu m'boma la Balaka | female |
|
M'modzi wa akuluakulu a msikawu a Emanuel Chilangwe wati kusamvana kwayamba chifukwa chakuti amalonda ochokera m'boma la Kasungu | M'modzi wa akuluakulu a msikawu a Imanuwelo Chilangwe wati kusamvana kwayamba chifukwa chakuti amalonda ochokera m'boma la Kasungu | female |
|
akugulitsa chimanga chawo pa mtengo wotchipa mosiyana ndi mtengo omwe akugulitsira amalonda a m'boma la Balaka omwe ndi wokwela | akugulitsa chimanga chawo pa mtengo wotchipa mosiyana ndi mtengo omwe akugulitsira amalonda a m'boma la Balaka omwe ndi wokwela | female |
|
Malingana ndi Chilangwe, amalonda a msika wa mangochi turn off akufuna anzawo obwerawa azipita kwawo ponena kuti akugulitsa chimanga pa mtengo wa k 39,000 kwacha | Malingana ndi Chilangwe, amalonda a msika wa mangochi theni ofu akufuna anzawo obwerawa azipita kwawo ponena kuti akugulitsa chimanga pa mtengo wa sate naini sauzande kwacha | female |
|
pomwe mavenda a msika wa Mangochi turn off mboma la Balaka akugulitsa pa mtengo wa 45000 kwacha zomwe iwo sakugwirizana nazo | pomwe mavenda a msika wa Mangochi theni ofu mboma la Balaka akugulitsa pa mtengo wa fote faifi sauzande kwacha zomwe iwo sakugwirizana nazo | female |
|
A polisi Ku Salima amanga a Tadeyo Juwawo a zaka 51 zakubadwa kaamba kopezeka ndi chamba opanda mapepala owayenereza | A polisi Ku Salima amanga a Tadeyo Juwawo a zaka fifite wani zakubadwa kaamba kopezeka ndi chamba opanda mapepala owayenereza | female |
|
Mneneri wa polisi ya Salima a Rabecca Ndiwate watsimikizira Times 360 Malawi kuti mkuluyu wagwidwa pa 1 February mma 2 koloko mmawa pomwe apolisi amachita chipikisheni pamalo akaphatenga m'bomali | Mneneri wa polisi ya Salima a Labeka Ndiwate watsimikizira taimusi fili sikisite Malawi kuti mkuluyu wagwidwa pa wanu febuluwale mma 2 koloko mmawa pomwe apolisi amachita chipikisheni pamalo akaphatenga m'bomali | female |
|
A Ndiwate ati woganiziridwayu anakwera galimoto lomwe limachokera ku Nkhotakota kupita kusalima ndipo apolisiwa atapeza chambachi anafunsa mwiniyu mapepala omuyenereza | A Ndiwate ati woganiziridwayu anakwera galimoto lomwe limachokera ku Nkhotakota kupita kusalima ndipo apolisiwa atapeza chambachi anafunsa mwiniyu mapepala omuyenereza | female |
|
kupezaka ndi katunduyu koma anakanika kutulutsa, zomwe zinachititsa kuti iwo amunjate Ndipo pakadali pano, a Juwawo akudikira kuti akaonekere kubwalo la milandu kuti akayankhe mlandu wopezeka ndi chamba opanda chilolezo | kupezaka ndi katunduyu koma anakanika kutulutsa, zomwe zinachititsa kuti iwo amunjate Ndipo pakadali pano, a Juwawo akudikira kuti akaonekere kubwalo la milandu kuti akayankhe mlandu wopezeka ndi chamba opanda chilolezo | female |
|
President wa timu ya Mighty Mukuru Wanderers a Thom Mpinganjira wati watopa ndi zindapusa zomwe timuyi yakhala ikupeleka kamba ka mchitidwe wa zipolowe pa masewero ena a timuyi | Pulezidenthi wa timu ya maite mukulu wandilazi a Thomu Mpinganjira wati watopa ndi zindapusa zomwe timuyi yakhala ikupeleka kamba ka mchitidwe wa zipolowe pa masewero ena a timuyi | female |
|
Mpondamatikiyu wati chaka chino, azipanga hayala apolisi a mfuti kuti azikhazikitsa chitetezo pa masewero okhudza timuyi | Mpondamatikiyu wati chaka chino, azipanga hayala apolisi a mfuti kuti azikhazikitsa chitetezo pa masewero okhudza timuyi | female |
|
Izi zadza kutsatira chindapusa cha K22 million chomwe timuyi adayilamula kuti ilipire yokonzetsera mipando ya pa bwalo la zamasewero la Bingu yomwe masapota ena a timuyi akuganiziridwa kuti anawononga | Izi zadza kutsatira chindapusa cha twente thu muliyoni chomwe timuyi adayilamula kuti ilipire yokonzetsera mipando ya pa bwalo la zamasewero la Bingu yomwe masapota ena a timuyi akuganiziridwa kuti anawononga | female |
|
Lawi, yemwe ali ndi zimbale zitatu- Sunset in the Sky, Thirties komanso Lawi, wati 'Solo' ndi nyimbo yake yoyamba chaka chino | Lawi, yemwe ali ndi zimbale zitatu- sani seti ini ve sikayi, fetezi komanso Lawi, wati 'Solo' ndi nyimbo yake yoyamba chaka chino | female |
|
Nyimboyi ndi yoitanira anthu kuti avine, chinthu chomwe thupi limakhumba mu nyengo yake."Kuvina n'kofunika, | Nyimboyi ndi yoitanira anthu kuti avine, chinthu chomwe thupi limakhumba mu nyengo yake."Kuvina n'kofunika | female |
|
koma timatero mu nyengo yake, watero Lawi za nyimboyi, yomwe yatuluka ndi kanema wake Lachinayi usiku | koma timatero mu nyengo yake, watero Lawi za nyimboyi, yomwe yatuluka ndi kanema wake Lachinayi usiku | female |
|
Iye anati kutuluka kwa nyimboyi ndi chiyambi cha ulendo wake wozukuta chimbale | Iye anati kutuluka kwa nyimboyi ndi chiyambi cha ulendo wake wozukuta chimbale | female |
|
M'malawi wina yemwe dzina lake ndi Kate Joyo watsekula malo odyera ku South Bend m'dziko la United States of America komwe akukhala | M'malawi wina yemwe dzina lake ndi Keti Joyo watsekula malo odyera ku saufi bendi m'dziko la yunaitedi sitetsi ofu amelika komwe akukhala | female |
|
Malo odyerawa anatsekulidwa ndi mfumu ya mzinda wa South Bend a James Mueller posachedwapa | Malo odyerawa anatsekulidwa ndi mfumu ya mzinda wa saufi bendi a jemusi mula posachedwapa | female |
|
A Joyo ati atsegula malo odyerawa ndi cholinga chopititsa patsogolo chikhalidwe cha ku Africa komanso kubweretsa pamodzi anthu aku Africa kuphatikizapo Malawi | A Joyo ati atsegula malo odyerawa ndi cholinga chopititsa patsogolo chikhalidwe cha ku Afilika komanso kubweretsa pamodzi anthu aku Afilika kuphatikizapo Malawi | female |
|
Tikuphika zakudya zaku Africa monga nsima, nsomba ya Chambo, ndi zina zambiri, atero a Joyo | Tikuphika zakudya zaku Africa monga nsima, nsomba ya Chambo, ndi zina zambiri, atero a Joyo | female |
|
Iwo ati anthu ambiri omwe akukhala kunja, amalakalaka atadya zakudya za kwawo koma samazipedza ndipo ndi chifukwa chake atsegula malowa | Iwo ati anthu ambiri omwe akukhala kunja, amalakalaka atadya zakudya za kwawo koma samazipedza ndipo ndi chifukwa chake atsegula malowa | female |
|
A Joyo ati ngakhale akukhala ku America ndi nzika ya Malawi kotero kuti kudzera mu malowa akukweza dziko la Malawi kumbali ya zokopa alendo | A Joyo ati ngakhale akukhala ku Amelika ndi nzika ya Malawi kotero kuti kudzera mu malowa akukweza dziko la Malawi kumbali ya zokopa alendo | female |
|
Apolisi ya Phalula m'boma la Balaka amanga abambo atatu powaganizira kuti amagulitsa feteleza wachinyengo wopangidwa kuchokela ku dothi, Lime komaso Terrazzo | Apolisi ya Phalula m'boma la Balaka amanga abambo atatu powaganizira kuti amagulitsa feteleza wachinyengo wopangidwa kuchokela ku dothi, Laimu komaso Telazo | female |
|
Mneneri wa polisi ya Balaka a Gladson M'bumpha, watsimikiza za nkhaniyi ndipo wati anthuwa ndi a Kawoja Madade a zaka 54, Lax Kapinga a zaka 35 | Mneneri wa polisi ya Balaka a Giladisoni M'bumpha, watsimikiza za nkhaniyi ndipo wati anthuwa ndi a Kawoja Madade a zaka fifite folo, Lakisi Kapinga a zaka fete faifi | female |
|
ndi a Enock Kazembe a zaka 39 onse ochokera kudera la mfumu yaikulu Phalula m'bomali | ndi a Inoki Kazembe a zaka fete naini onse ochokera kudera la mfumu yaikulu Phalula m'bomali | female |
|
Malingana ndi a M'bumpha, anthuwa agwidwa patachitika kafukufuku potsatira madandaulo a anthu ena m'derali kuti anthu ena akugulitsa feteleza yemwe sali wovomelezeka | Malingana ndi a M'bumpha, anthuwa agwidwa patachitika kafukufuku potsatira madandaulo a anthu ena m'derali kuti anthu ena akugulitsa feteleza yemwe sali wovomelezeka | female |
|
Atatuwa akaonekela ku bwalo la milandu posachedwapa komwe akayakhe mlandu opanga komaso kugulitsa feteleza wachinyengo | Atatuwa akaonekela ku bwalo la milandu posachedwapa komwe akayakhe mlandu opanga komaso kugulitsa feteleza wachinyengo | female |
|
Pamene boma ndi mabungwe omwe sali a boma akuyesetsa kulimbana ndi imfa za makanda m'dziko muno, pakuonesetsa kuti mwana aliyense akulandira chithandizo cha zaumoyo | Pamene boma ndi mabungwe omwe sali a boma akuyesetsa kulimbana ndi imfa za makanda m'dziko muno, pakuonesetsa kuti mwana aliyense akulandira chithandizo cha zaumoyo | female |
|
Times 360 Malawi yepeza kuti ana ochokera kwa Kaputalambwe, m'dera la mfumu yayikulu Mkukula m'boma la Dowa akulephera kupeza chithandizochi kamba ka kuonongeka kwa mlatho wa Nkhondodwa m'bomali. | Taimusi fili sikisite Malawi yepeza kuti ana ochokera kwa Kaputalambwe, m'dera la mfumu yayikulu Mkukula m'boma la Dowa akulephera kupeza chithandizochi kamba ka kuonongeka kwa mlatho wa Nkhondodwa m'bomali. | female |
|
Mkhalapampando wa Kaputalambwe Mother Care Group mayi Annie Jana wauza Times 360 Malawi kuti iwo ndi odandaula kwambiri ndi vuto la mlatho umenewu | Mkhalapampando wa Kaputalambwe Mava keya gulupu mayi Ani Jana wauza Taimusi fili sikisite Malawi kuti iwo ndi odandaula kwambiri ndi vuto la mlatho umenewu | female |
|
gulu lawo layesetsa kukumana ndi adindo osiyanasiyana kudelari kuti achitepo kanthu mwansanga koma madadaulo awo sakuphula kanthu | gulu lawo layesetsa kukumana ndi adindo osiyanasiyana kudelari kuti achitepo kanthu mwansanga koma madadaulo awo sakuphula kanthu | female |
|
Mmodzi wa akuluakulu a bungwe la Malawi Health Equity Network a Bishop Mophat Litchapa wati izi ndi zodandaulitsa kwambiri | Mmodzi wa akuluakulu a bungwe la Malawi Hefe ikwite netiweki a Bishopu Mofati Litchapa wati izi ndi zodandaulitsa kwambiri | female |
|
kuona kuti ana ena ufulu wawo wolandira chithandizo cha chipatala ukukanidwa ndipo iwo apempha amayiwa kuti asasiye kugogoda ku ma ofesi a adindo m'bomali | kuona kuti ana ena ufulu wawo wolandira chithandizo cha chipatala ukukanidwa ndipo iwo apempha amayiwa kuti asasiye kugogoda ku ma ofesi a adindo m'bomali | female |
|
Ndikudziwa azimayi akuvutika kuti ana azikalandira kuchipatala kutali, mlatho umeneu umawathandiza mayendedwe ndipo ngati ine mzimayi mzawo zikumandikhudza | Ndikudziwa azimayi akuvutika kuti ana azikalandira kuchipatala kutali, mlatho umeneu umawathandiza mayendedwe ndipo ngati ine mzimayi mzawo zikumandikhudza | female |
|
n'chifukwa ndayesetsa kupeza ndalama kuti alikonze msangansanga," atero a Daudi | n'chifukwa ndayesetsa kupeza ndalama kuti alikonze msangansanga," atero a Daudi | female |
|
A Daudi ati iwo akuchita zothekera zonse kuti mlathowu ukonzedwe mwachangu, ndipo anenanso kuti mlathowu ukhala utakonzedwa pofika mwezi wa December chaka chomwe chino cha 2024 | A Daudi ati iwo akuchita zothekera zonse kuti mlathowu ukonzedwe mwachangu, ndipo anenanso kuti mlathowu ukhala utakonzedwa pofika mwezi wa Disemba chaka chomwe chino cha twente twente folo | female |
|
Kodi tingatani ngati dziko kuti pazikhala ubale wabwino pakati pa mtsogoleri wa dziko ndi wachiwiri wake, Osaiwala kutchera Wayilesi ya Times nthawi ya 5:00 madzulo, kuti mumvere pologalamu ya Times Talk | Kodi tingatani ngati dziko kuti pazikhala ubale wabwino pakati pa mtsogoleri wa dziko ndi wachiwiri wake, Osaiwala kutchera Wayilesi ya Taimusi nthawi ya faifi koloko madzulo, kuti mumvere pologalamu ya taimusi thoko | female |
|
Anthu a m'midzi ya Makandika komanso Nthiko m'boma la Machinga kumasanaku anatseka msewu wa Zomba-Liwonde pamalo otchedwa Mpita | Anthu a m'midzi ya Makandika komanso Nthiko m'boma la Machinga kumasanaku anatseka msewu wa Zomba-Liwonde pamalo otchedwa Mpita | female |
|
ati pofuna kukakamiza akuluakulu a ofesi yoona za nkhalango m'bomali kuti amasule anthu asanu omwe ofesiyi inawagwira akudula mitengo yootchera makala mu nkhalango yotetezedwa ya Makandika Nkula | ati pofuna kukakamiza akuluakulu a ofesi yoona za nkhalango m'bomali kuti amasule anthu asanu omwe ofesiyi inawagwira akudula mitengo yootchera makala mu nkhalango yotetezedwa ya Makandika Nkula | female |
|
Izi zinakwiyitsa anthuwa omwe anatchingira galimoto lomwe akuluakulu oona za nkhalangowa anakwera pomwe anatchinga msewuwu ndi mitengo komanso kuyatsa mateyala | Izi zinakwiyitsa anthuwa omwe anatchingira galimoto lomwe akuluakulu oona za nkhalangowa anakwera pomwe anatchinga msewuwu ndi mitengo komanso kuyatsa mateyala | female |
|
Wofalitsa nkhani za polisi ya Machinga Western Kansire wati apolisi anathamangira ku malowa, komwe anakwanitsa kubalalitsa gulu la anthu okwiyawo pogwiritsa ntchito utsi wokhetsa misozi | Wofalitsa nkhani za polisi ya Machinga Wesiteni Kansire wati apolisi anathamangira ku malowa, komwe anakwanitsa kubalalitsa gulu la anthu okwiyawo pogwiritsa ntchito utsi wokhetsa misozi | female |
|
Malingana ndi a Kansire, asanuwa, omwe ndi a Mussa Janatu azaka 35, Stuward Macheza azaka 29 | Malingana ndi a Kansire, asanuwa, omwe ndi a Musa Janatu azaka sate faifi, Situwati Macheza azaka twente naini | female |
|
Snever Henderson azaka 24, Rabecca Tiyesi azaka 21 ndi a Violet Amidu azaka 21, ali m'chitokosi cha apolisi | Siniva Hendesoni azaka 24, RabekaTiyesi azaka 21 ndi a Vayoleti Amidu azaka 21, ali m'chitokosi cha apolisi | female |
|
Pakadali pano, bata abwelera ndipo galimoto zayamba kudutsa mu msewuwu | Pakadali pano, bata abwelera ndipo galimoto zayamba kudutsa mu msewuwu | female |
|
Nduna ya zachitetezo a Harry Mkandawire yati siikudziwapo kalikonse za kuopsyezedwa kwa mtolankhani Gregory Gondwe kutsatira nkhani imene adalemba | Nduna ya zachitetezo a Hale Mkandawire yati siikudziwapo kalikonse za kuopsyezedwa kwa mtolankhani Giligole Gondwe kutsatira nkhani imene adalemba | female |
|
Yomwe idaulula kuti boma likuperekabe ndalama ku kampani ya a Zuneth Sattar pa kontalakiti yomwe idathetsedwa ndi mlangizi wamkulu wa boma pa nkhani ya malamulo a Thabo Chakaka Nyirenda | Yomwe idaulula kuti boma likuperekabe ndalama ku kampani ya a zunefi sata pa kontalakiti yomwe idathetsedwa ndi mlangizi wamkulu wa boma pa nkhani ya malamulo a Thabo Chakaka Nyirenda | female |
End of preview. Expand
in Data Studio
No dataset card yet
- Downloads last month
- 52