audio
stringlengths
43
45
text
stringlengths
0
24.1k
start_time
int64
0
1.83k
end_time
float64
1.74
1.85k
./data/chichewa-dataset\audio\segment_101.wav
Basi kagoneni, mawa paja ndi la sukulu Basi kagoneni, mawa paja ndi la sukulu
0
5.44
./data/chichewa-dataset\audio\segment_102.wav
Malume zilibwino kwambiri Malume zilibwino kwambiri
0
5.056
./data/chichewa-dataset\audio\segment_103.wav
Kakuoneka kuti kakomatu ka series kamenekaKakuoneka kuti kakomatu ka series kameneka
0
6.08
./data/chichewa-dataset\audio\segment_104.wav
Katundu uja mpakana panoKatundu uja mpakana pano
0
4.352
./data/chichewa-dataset\audio\segment_105.wav
Katundu afika liti?Katundu afika liti?
0
4.288
./data/chichewa-dataset\audio\segment_106.wav
Mwanyamuka?Mwanyamuka?
0
4.608
./data/chichewa-dataset\audio\segment_107.wav
Ndine chikanda ndimafuna kuti tilankhulaneNdine chikanda ndimafuna kuti tilankhulane
0
6.08
./data/chichewa-dataset\audio\segment_108.wav
Zikomo kwambiri phone yafika pano ili ku ChancoZikomo kwambiri phone yafika pano ili ku Chanco
0
5.503188
./data/chichewa-dataset\audio\segment_109.wav
Kodi amwene mwafika?Kodi amwene mwafika?
0
5.952
./data/chichewa-dataset\audio\segment_110.wav
Ndimayenela kunyamuka dzana waku Rwanda koma ndinadwala COVID. Ndimayenela kunyamuka dzana waku Rwanda koma ndinadwala COVID.
0
5.45675
./data/chichewa-dataset\audio\segment_111.wav
Nde ndamuuza anditumizile ine, ndekuti utha kungopanga invoice ya $2500. Nde ndamuuza anditumizile ine, ndekuti utha kungopanga invoice ya $2500.
0
9.079063
./data/chichewa-dataset\audio\segment_112.wav
Kapena ndizapange deposit yokwana 2000$Kapena ndizapange deposit yokwana 2000$
0
4.620813
./data/chichewa-dataset\audio\segment_113.wav
Kodi za ndalama zija alipo angandilipirire 2000$ ndimpatse ma kwachaKodi za ndalama zija alipo angandilipirire 2000$ ndimpatse ma kwacha
0
6.03725
./data/chichewa-dataset\audio\segment_114.wav
Mmawa uno atha kukatengaMmawa uno atha kukatenga
0
3.018625
./data/chichewa-dataset\audio\segment_115.wav
Unakumana naye mamuna wa Nia?Unakumana naye mamuna wa Nia?
0
3.901
./data/chichewa-dataset\audio\segment_116.wav
Nde yama diaper ija munditumizila week yammawaNde yama diaper ija munditumizila week yammawa
0
3.71525
./data/chichewa-dataset\audio\segment_117.wav
Phone yabwino ndalama zingatiPhone yabwino ndalama zingati
0
3.041875
./data/chichewa-dataset\audio\segment_118.wav
Chawezi zoona izi? Mwayamba kulemba tiana tu?Chawezi zoona izi? Mwayamba kulemba tiana tu?
0
4.29575
./data/chichewa-dataset\audio\segment_119.wav
koma abale anzanga zinthu zake phone ija nde yasokonekeleratu ayi zimachitikakoma abale anzanga zinthu zake phone ija nde yasokonekeleratu ayi zimachitika
0
8.9165
./data/chichewa-dataset\audio\segment_120.wav
Avomere basi kuti zitengera eni akefe kufuna apo biii azichita kugwadaAvomere basi kuti zitengera eni akefe kufuna apo biii azichita kugwada
0
5.108438
./data/chichewa-dataset\audio\segment_121.wav
Kodi ndiye azawatolera motani ma loan wa koma? Kodi ndiye azawatolera motani ma loan wa koma?
0
4.690438
./data/chichewa-dataset\audio\segment_122.wav
Mpamene pataulurike zonse apapa, amaba misonkho.Mpamene pataulurike zonse apapa, amaba misonkho.
0
4.527938
./data/chichewa-dataset\audio\segment_123.wav
Okathandizira kugawa tilipo ambiri masanawadi.Okathandizira kugawa tilipo ambiri masanawadi.
0
5.688938
./data/chichewa-dataset\audio\segment_124.wav
Zikomo kwambiriZikomo kwambiri
0
2.670313
./data/chichewa-dataset\audio\segment_125.wav
Eyadi, tonse zitikwane basi.Eyadi, tonse zitikwane basi.
0
4.017063
./data/chichewa-dataset\audio\segment_126.wav
mudzawona ngati moyo ngophweka...mudzawona ngati moyo ngophweka...
0
3.529438
./data/chichewa-dataset\audio\segment_127.wav
Malume panongo zinthu sizikuyenda osati sewelo.Malume panongo zinthu sizikuyenda osati sewelo.
0
5.317375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_128.wav
Chaka Chiko mvula yagwa mowononga zinthu, mpaka napolo ku chikwa ndi nsanjeChaka Chiko mvula yagwa mowononga zinthu, mpaka napolo ku chikwa ndi nsanje
0
6.176563
./data/chichewa-dataset\audio\segment_129.wav
Ngati mupitilize nkhalidwe wanuwo moyo wanu simupita patali.Ngati mupitilize nkhalidwe wanuwo moyo wanu simupita patali.
0
4.806563
./data/chichewa-dataset\audio\segment_130.wav
Kwezani mowa tsitsani mafuta ophikila chondeKwezani mowa tsitsani mafuta ophikila chonde
0
5.363813
./data/chichewa-dataset\audio\segment_131.wav
Lero ndiye tiumwa mowa kwabasi.Lero ndiye tiumwa mowa kwabasi.
0
3.784875
./data/chichewa-dataset\audio\segment_132.wav
Koma aise ukununkha kwambiri, koma wasamba?Koma aise ukununkha kwambiri, koma wasamba?
0
5.108438
./data/chichewa-dataset\audio\segment_133.wav
Mkamwa mwako mukununkhaMkamwa mwako mukununkha
0
3.761688
./data/chichewa-dataset\audio\segment_134.wav
Amayi ndi abambo ako adusa pompano akupita ku msika.Amayi ndi abambo ako adusa pompano akupita ku msika.
0
5.03875
./data/chichewa-dataset\audio\segment_135.wav
Anzanthu mwatchenatu zovala zokongola, akugulirani ndani?Anzanthu mwatchenatu zovala zokongola, akugulirani ndani?
0
5.03875
./data/chichewa-dataset\audio\segment_136.wav
Zimakhala zonvesa chisoni kwambiri pamene wataya wokondedwa wako.Zimakhala zonvesa chisoni kwambiri pamene wataya wokondedwa wako.
0
4.87625
./data/chichewa-dataset\audio\segment_137.wav
Ndikunva maluno mthupi.Ndikunva maluno mthupi.
0
3.738438
./data/chichewa-dataset\audio\segment_138.wav
Madzi akatentha mundiyitane ndizasambe.Madzi akatentha mundiyitane ndizasambe.
0
4.040313
./data/chichewa-dataset\audio\segment_139.wav
Inu mukuona ngati zikamatha zaka 10 moyo wanu ukhala wosinthika?Inu mukuona ngati zikamatha zaka 10 moyo wanu ukhala wosinthika?
0
6.664188
./data/chichewa-dataset\audio\segment_140.wav
mmene munayambila muja mavuto amenewa azakuthelani koma, kapena tiziti alipo anakutembelerani.mmene munayambila muja mavuto amenewa azakuthelani koma, kapena tiziti alipo anakutembelerani.
0
8.289563
./data/chichewa-dataset\audio\segment_141.wav
Bread uja sikuti angokweza mtengo kokha atchotsamonso ma slice awiri Bread uja sikuti angokweza mtengo kokha atchotsamonso ma slice awiri
0
6.339063
./data/chichewa-dataset\audio\segment_142.wav
Mmoya wanga wnse mvula sinagwepo mochuluka chonchi, mwina dziko likutha.Mmoya wanga wnse mvula sinagwepo mochuluka chonchi, mwina dziko likutha.
0
7.035688
./data/chichewa-dataset\audio\segment_143.wav
Pamene ali iye uja ali ndi zibwenzi zisanu kuphatikiza akazi anayi. munthu amene uja ndi hule ndithu.Pamene ali iye uja ali ndi zibwenzi zisanu kuphatikiza akazi anayi. munthu amene uja ndi hule ndithu.
0
9.10225
./data/chichewa-dataset\audio\segment_144.wav
Tiyeni tilimbikile kulima chimanga mwina tikhonza kukolora zochuluka ndikupedza ndalama.Tiyeni tilimbikile kulima chimanga mwina tikhonza kukolora zochuluka ndikupedza ndalama.
0
6.292625
./data/chichewa-dataset\audio\segment_145.wav
Amene sanasonkhe nawo sadya mmemo.Amene sanasonkhe nawo sadya mmemo.
0
3.947438
./data/chichewa-dataset\audio\segment_146.wav
Mu dziko lathu panopa chili chonse chakwera. katundu akudula mopitilira muyezoMu dziko lathu panopa chili chonse chakwera. katundu akudula mopitilira muyezo
0
5.2245
./data/chichewa-dataset\audio\segment_147.wav
Lero ndiye mwatchena asisi, zimenezi mwagula ku mbeya?Lero ndiye mwatchena asisi, zimenezi mwagula ku mbeya?
0
4.249313
./data/chichewa-dataset\audio\segment_148.wav
Awa ndi makulina akulu, chombo cha p anseu.Awa ndi makulina akulu, chombo cha p anseu.
0
4.342188
./data/chichewa-dataset\audio\segment_149.wav
Malaya awa akundithina kwambiri makamaka mimba yangayi yakula kwambiri.Malaya awa akundithina kwambiri makamaka mimba yangayi yakula kwambiri.
0
5.526375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_150.wav
Ku ntchito sindipitako ndadwala.Ku ntchito sindipitako ndadwala.
0
2.92575
./data/chichewa-dataset\audio\segment_151.wav
Mayi ake ndiovuta kwambiri, anayamba apenga misala ali mwana.Mayi ake ndiovuta kwambiri, anayamba apenga misala ali mwana.
0
4.551125
./data/chichewa-dataset\audio\segment_152.wav
ife kuno tilibwino tose zikomoso nanu kuti muli bwino eya achikambe nawo ah alibwino indetu kulima masiku ano mabize mabize zikomo zikomo
0
17.664
./data/chichewa-dataset\audio\segment_153.wav
Ndachoka pang'ono, ndikubwela, ndikubwela pompano.
0
4.864
./data/chichewa-dataset\audio\segment_154.wav
ati a ati amakaikila ama amona ngati kuti mwina tungo mdoja kuti mwina mpandowo ungojambulidwa sukupangidwa and then nde eh atauona kunali ku ukhalilatu akangotele eh naisi chair akangotele nice chair ndamuuza kuti aha tapanga mani ndumenewotu mukanika nokha chifukwa choti mtengo sitikuvana hehe
0
30
./data/chichewa-dataset\audio\segment_155.wav
30
33.792
./data/chichewa-dataset\audio\segment_156.wav
inde ndili ku mzuzu ndabwela kodi ndabwela liti lasti ofu lasti wiki eh mna mnapeza ka ga ganyu mmalowetsa data nde nabwela chifukwa cha zimenezo nde basi ndangomkhalilatu e
0
20.650688
./data/chichewa-dataset\audio\segment_157.wav
ah ife tili bwino kuno zoipa mzomwezi za dzanjai izi kuno koma achikambe nde eh mmimba kutsegula kamwazi eyetu kaya odwala waja azione aliko bwanji pano
0
14.506688
./data/chichewa-dataset\audio\segment_158.wav
aise ndine lameck tu kuli bwanji kumeneko muli ku lilongwe kapena ku mzuzu tasimbani za moyo braz
0
12.288
./data/chichewa-dataset\audio\segment_159.wav
Dzina langa ndine Carlo Beya, interview number one community leader, Nsangwa village T/A Kayembe Dowa. Tikuyamba!! Choyamba ndufuna ndidziwe kuti inu mudzi muno muli ndi udindo wanji? Ah Choyamba ndufuna ndidziwe kuti inuyo mudzi muno muli ndi udindo wanji? Ineyo mudzi muno ndili ndi udindo monga ku khola la za ngÕombe za backing group ndine treasure wa mudzi muno, treasure wa backing group ya Talandira Kayembe Basa backing group ndine treasure. Oho? Eya. zikomo kwambiri. Paliso udindo wina omwemuli nawo kupatula umenewo? Udindo wina wa mudzi muno, ndine tsogoleri wa ku azimayi monga azimayi a bank nkhonde ndine treasures so ku bank nkhonde. Mmm ho, eya. Zikomo kwambiri. Bank nkhonde imeneyi Dzina lake timati Tidziwane bank nkhonde, ohoo, eyaaa. Tidziwane bank nkhonde imeyi ndi yaa anayambitsa mudzi muno ndi abungwe lanji? A CARE. Oho, eyaa, zikomo kwambiri. Nthawi imeneyi imayamba ineyo ndidali VA eya, oho, wochokera ku CARE komweko. Oho, Tinali ndi alangizi aja anyamata amati anajimmy panthawi imeneyo kuchokera 15 kubwera kulekeza chaka chathachi ndiye atisintha kuti kufunika ena a malangizi. Mukati munali VA mukutantahuza kuti munali ndani? Mlangizi wakumudzi, oho, mlangizi wakumudzi, oho, wamagulu, ndimayendera magulu ten, ah ooho, ndithudi. Magulu ten wa amudzi momuno? Ayi, ndinali magulu munomo munali magulu five ndekuti madera enawa kunali magulu five monga kondendera, kotsala, kogalanga eya. Zikomo, ndithu. Inuyo mwakhala mutengapo gawo mwina mongowonjera mwakambako zoti mwakhalako treasure wa za bank nkhonde, mwakha treasure komaso ku za bank za ngÕombe, chinaso mwakhala mutengako gawo ku chitukuko chokhudza ndi project ya CARE imeneyi ndi chani? Chitukuko cha puloject ya CARE, mm ndinatengako mbali monga ndinali mphuzitsi wa tiwana tingÕno tingÕono iti ta nursery school ndimatiphunzitsira pomwepa apapa. Oh panyumba panu pompano? Ndithu tere, ndinatengako gawo liemeneli zedi. Nde kuwaphunzitsako mukupitiriza? Ndingofuna tivetsetse kuti? Panopa ndidasiya chaka chathachi, kuti ndisiye chaka chathachi ndidanena kuti, makolo adule mitengo amange ka mpanda koti nidzikhalamo ndi wanawa. Mm, nde makolo ena adachilora koma makolo ena sadachilore nde ndidakana kuti sinanga ndi kwamvula nde nthawi ino ya mvula ino ana amanyowa. Nde masiku ambiri kukachita mvumbi samabwera ku school nde ndidafuna kuti ayike kampanda navika naikapo pepala nde makolo ena dalora koma makolo ena sadachilore koma Chaka chathachi nasiya pa mwezi wa mariachi, ndithudi. Anawa akabwera kudzaphunzira kunoko aah malipiritsa kena kake kapena zimakhala bwanji? Ayi anawo sinimalipiritsa kabwera kuno ku school ndimaphunzitsa nde ndimawauza makolowo amasonkhana sonkhana chimanga mkukagaya nde timaphika phala eya. Timatengako makolo ena tsiku lina adzaphika, tsiku lina ena aphike ndi makolo ena, akati chimangacho alibe amango gula sugar mapaketi angapo basi mkuphika tea kumawapatsa ana aja timagula zigumu ndithudi, ayi Zikomo kwambiri. Aaah china chomwe timafuna tiphunzire nawo tidziwe ndichokhudzana ndi ngati inuyo kukhala tsogoleri wa mudzi? Ndi zikhulupiriro zitizo dera munomo zomwe anthu amakhulupirira? Eee dera muno kapena ndinene kuti kudera kuno kwa Kayembe, zikhulupiriro zambiri zimene anthu amazikhulupirira masiku awowo kusanabwere CARE kunali za chipati kuti mamuna akamwalirira amakalowa chipati. Monga mene ndiliri ineyo amuna wanga akamwalirira ndekuti achibale awo alowe chipati kwa ine, zikhulupiriro zimenezi zinalipo, komaso kunali zikhulupiro zoti munthu ngati ali ndi pakati asadye dzira angakaone mwana wa dazi, komaso asadye mzimbe angakaone mwana wa mfundu zambiri, zikhulupiriro zimenezo mu dera muno zinalipo koma mene yabwera CARE ndi maphunziro nduona kunena kuti zikhulupiriro zimenezozo zachepa kwambiri, tsopano tili pa nzere owona zomwe CARE ikutiphunzitsa kuti chili chose ndi chofunika munthu azidya akakhala oyembekezera, ndithudi. Ndingofuna ndivetsetse mwati kulowa zipati mukutanthawuza chani? Eyaaa kulowa chipati kumakhala ngati mamuna uja wamwalirira iweyo ulipomwepo achibale ndiye ena amene sa achibale ake omwe amakufuna akhaleso amuna wako eyaaa nde amati chipati masiku amenewowo, koma ndimene yabwerera maphunziro anu mubwerera nawo a CARE ndikuona kuti zachipatizo zachepa. Amati kulowa chipati, kuthyola fumbi mwina akakhalapo anthu five osewa amathyola masekera mwina amakhalapo ten nde iweyo ukawerenge masekerawo nde matsekera omwe utsirizire kuwerenga ukamukonda munthuyo umasunga masekera amenewo kuti ineyo andilowa chipati ndi uyu, koma zimenezi zachepa ndimaphunziro omwe tilu panganga masiku ano, ndithudi. Zikomo , Zikomo kwambiri. Nde zikhulupiliro zomwe mwalongosolazi ndimati ndi zikhulupiriro zomwe mwalongosolazi zimakhudzana bwanji ndi maudindo amayi ndi abambo? A chipatiwo kapena? Kapena zachiaptizo kapena zamadyedwe mene mumalongosoloera kuti mzimayi akakhala ndi pakati samaloredwa kudya mazira ndimangofuna ndingovetsetsa kuti zimakhudzana bwanji ndi amudindo amayi ndi abambo ku nkhanaiso yokhudzana ndi kadyedwe kabwino? Monga mene nanera kuti munthu akakhala odwala asadye dzira ndekuti chikhulupiriro chimene chija chimayambira mbanja, mwakho lake la bamboo uja eyaaa ndekuti amayamba zimenezo nde kuti ndi kholo lake la bamboo yo kumuwuza kuti kazi wako dzira ayi, mzimbe yayi sinanga ndekuti iwe ndi mtengwa umavera ziti?!! Zimene bamboo alikunenayo masiku amenewowo, koma masiku anowa timaona kuti bamboo wene weneyo ndiye amakagula mazira kukapatsa mayi kuti phikani mudye, eeh ndiye amakatenga mzimbe idzyani. Ngakhale nthochi yeni yeniyo amamuletsa mayi akakkhala oyembekezera asadye ati mwana amadzakhala otuwa muja ituwira nthochi. Nde zimenezozo masiku amenewowo chidali chiziko ndithu chapa banja chifukwa cha makolo omwe adalipo. Koma lero zaka zimene munangoti mwabweretsa maphunziro ayini ake awa komaso kunoko timatha timathokoza kwambiri mlangizi wathu Lufeyo chifukwa mayesetsa kuphunzitsa khomo ndi khomo amayenda ndithu khomo ndi khomo, moti chabe zimangokhala kuti munthu nga si munthudi munthu ati amaiwala mwina zambiri zimene munthu ali kumphunzitsa chifukwa ambiri ndife osamphunzira ambiri ndi ophunzira koma kuti ugwire chinthu chija ngakhale iwe ophunzira koma mwina china chimakutani? chimakutani? Chimakuthawa, koma nyamata ameneyu amayesetsa mdera linolo, timuthokoze kwambiri pa zomwe mumamutuma amayesetsa, Zikomo kwambiri, ndithudi. Ndimafuna ndidziwe kuti pa zikhulupiro munanenzi ndi ziti zomwe zimaoneka kuti anthu akudzikhulupirirabe akukhudzana ndi ujeno zoyenera kuti anthu azizichita? Zikhulupiriro zimenezo pali pano zidachepa, wanthu Sali zufunaso ayi na ma banja amasiku anowa sizuli funika ayi, ndimapunziro amene tulandira ndipo munthu sangazikhulupirireso ayi komaso khangakhale mamuna sangalore kuchita zikhulupiriro ngati zimenezi chifukwa zimenezo zidapita ndi makolo yathu ndi tsamunda pamene maphunziro ayambika ifeyo tukhulupirira kwambiri pa ziphunzitso zomwe muli kutiphunzitsa amabungwe, amabungwe osiyana siyana kuonjerapo CARE yu, tili zikhulupiriro zomenezi kuti zikhulupiriro zimenezo aah sizingakhaleso zokhulupirika kweni kweni tsopano ku wanthu. Zikomo kwambiri. Aah pazaka zitatu zimene bungwe liemeneri lakhala lugwira ntchito mudera munomo ndi zinthu ziti zomwe inuyo mwaona kuti ntchito imeneyi zapindula? Oho pa ntchito yakhala ikuchitika pa zinthu zimenezi pa zaka zitatu, nctchito yonena kuti asula wanthu ma banja dera lathu lino komaso atiphunzitsa kuti tidzikhala magulu yakusunga ndi kubwereketsana, magulu amenewa ni magulu oti ali kuthandiza kwambiri pa zinthu zina kusiyana kuti munthu atenge ndalama akaike ku bank mwina walandira zinthu nusiku za zidzidzi amangopita ukoko ,mkukabweraka ndalama ija ali kunyamuka ni mwana ulendo wakuchipatala. Zikuthandiza kwabasi kusiyana ndi kuti munthu anyamuke pano apite ku bank ku Mponela nanga mwanayo adzamupeza ali bwanji? Chifukwa masiku ano kudwala kwa ana alikwangothamangira kukomoka ndiye ndalama za bank nkhonde ndi mene anatiphunzitsira CARE zili mkuthandiza kwabasi chifukwa zili kwa mkuno kumudzi, oho zili kuthandiza kwabasi, komaso ndi zitukuko zambiri zimene zili kuchitika mwabwera nazo inu a CARE pomatiphunzitsa monga masamalidwe yapakhomo, komaso kasamalidwe ka bapabanja pathupano monga wana, madyedwe abwino kuti tidzidya zinthu zakasintha sintha. Pali zinthu zambiri zakasintha sintha zimene timadya mwina pali magulu six koma mwina sitingakwaniritse kukwanitsa magulu six wo patsiku komatu mwina timadyako atatu, mwina anayi patsiku eyaa. Monga ku dzakudya dzokhutitsa izi kugulu la nsima, nthochi za ziwisi zophika ndiye kuti kuli zamafuta monga umwako ka mkaka aka ndiye kuti zamafuta zi mukhoza kukanga mafuta ya nyamaya mukaphika, mukagula nyama ndiye kuti zosezi zikukhala magulu yatii, mutengako tisinjiro ndikuthira kuphala kuti zakudya amaguluwo tilu chita ndithu koma sitingakwanitse sinanga pakuti kuno ndi kumudzi, mmh, ndithu. Zikomo kwambiri, mongowonjezera ndi zinthu ziti pa zomwe mwakambazi zinaso zomwe zasintha mudzi muno mu zaka zitatu zimenezi mene kunabwera bungwe liemeneri? Kumbaliso zokhudzana ndi maudindo amayi ndi abambo? Zinthu zimenezi zasinthadi, kale ma udindo amangotengana abambo koma monga mene zakhalira masiku yano pamaphunziro amene tililuarandira monga mudzi mwathu muno, tili ndi VA, kapena tinene kuti VDC chairman wake ndi mzimayi muno mwathu muno, Komaso tili ndi drawo mipando yochuluka chairman, treasure, secretary ndi mzimayi. Azibambowa ali kungotsatira ma commit zinthu zoti zili ku sintha ndithu kunalibe komaso tili ndi kuthokoza kwabwino maka maka ku nkhani ya dirawo chifukwa kale timalimbirana ndi ngÕombe madzi pa chitsime, ngombe zumwapo ife tukatunga madzi madzi ndiye chimenechi tuthokoza kwambiri kuti zinthu zipita kasintha monga mudzu wathu uno kapena dera lathu lino. Mzimayi ndiye tsogoleri ndithu wa VDC Mukuona kuti zinthu zasintha chiomwe chigfukwa chani? Zasintha chomwechi chifukwa chamaphunziro omwe alikubwera ndi ma bungwe osiyana siyana, chifukwa kale kudalibe zimenezi. Zasintha ndithu maka inu a CARE muli kukhalapo ndi chidwi kwambiri pamaphunziro amenewawa. Zasintha ndithu kale kudalibe zimenezizo, kunalibe ndithu. Ineyo ndakhalapo ndithu mkanthawi pamudzi panopa, pamudzi ndabwera ndithu mkanthawi pamudi panopa koma zambiri zidali zotsalira, koma pamene kuli kubwera ma bungwe osiyana siyana nuona kuti zinthu zatukuka kwambiri, zatukuka kwambiri, mhu, ndithudi. Oh Zikomo nanga potengera nkhani yokhudzana ndi kadyedwe kabwino kapenaso ma udindo amene amakhalapo pakati pa amayi ndi abambo aaaah zomwe anthu mudera munomo amapanga mm? mwina ngati kupamga ngati nthawi ndi nthawi zokhudzana ndi madyedwe abwino zomwe amapanga anthu mudera muno ndi zitizo? Kapena kuzitsatira? Eyaaa , zokhudzana ndi madyedwe abwino ngakhaleso ma udindo amayi n di abambo? Zimenezi timazitsatira maka maka masiku anowa za madyedwe abwino ambiri akuzitsarira chifukwa tuyika timadimba makomo eya timabyalamo timbeu tosiyana siyana ndiye kuti tiakona kuti zina zina zatisoweka timayesetsa ndithu kuyenda komaso, mudzi munomu azimayi atengapo mbali kwabasi po mageni omakatenga nsomba kochimwaza kumabwera nazo , tomato namadzagulitsa mudzi muno nde madyedwe abwino sakukhalaso otarimphira ayi komaso mwini khomo titha kunena kuti madyedwe abwino ali kuchitika mudzi munomo kapena nene kuti mu dera linoli chifukwa ngakhale chalo chimene amati akapita mafumu amawauza kuti madyedwe abwino abwino pakhomo lamunthu asamataliphira ayi ndiye konzani madimba nde timadimbapo timakonza ndithu. Zikomo kwambiri. Nanga kumbali yakuti pa zomwe zasintha pa zaka zitatu zimenezizi mmh momwe project imeneyiyi inayamba kugwira ntchito mudera muno , zomwe mukuona kuti zasintha Kumbaliso yokhudzana ndi abambo ndi amayi kumbali yakadyedwe mukona chasintha ndi chani kupatula komwe munena kuti mwapanga madimba anthu malo moti mukagule masamba mumathyola pa dimba panu. Chinaso chomwe mukuona kuti chasintha ku mbali yakadyedwe ngakhaleso maudindo kumbali ya kadyedwe komaso ma udindo ndi chani? Mmh chimene chasintha pakadweke ndikukhalirana limodzi ndi abambo monga kumapangana zochita kuti pakakhala ndalama iyi tiyione kuti ndalama yi ilibwanji chifukwa kale zabanja kuti ayi ndalama zitere tere mayi wanga sizimakhala lamulo lidali la abambo okha. Ngakhale mayi ali kulamulapo pankhani ya ndalama, kuti aaah ndalama ndi zimenezi tazipezeza tiguleko chakuti tiguleko chakuti pakhomo pano pafunika zakuti monga wana madyedwe abwino ngofunika kuti mwana asamanyentcherere, nde tili kutenga nawo mbali, zinthu zimenezi zasintha zedi chifukwa kale sitimaziona. Mukuona ngati kale sizimachita choncho chifukwa chani? Tsano kale udindo unali wa bamboo yekha. Akpeza ndalama zoti akhoza kuwuza mayi kuti nda;lama ndi izi kunalibe. koma chifukwa chamaphunziro omwe ali kubwera kutsogoloko tuona kuti zinthu zasintha zedi zasintha zedi. Ngakhale ma banja awana awa ali osangalala zedi chifukwa chamaphunziro omwe ali kuchitika kawiri kawiri , zosintha zedi madyedwe abwino ali palipose khomo ndi khomo ndithudi, Zikomo kwambiri. Aaah mungatiuzeko kuti kupatulako project iyiyi ya CARE mudzi munomo iliposo project ina yomwe mwina imaphunzitsa za kadyedwe kabwino? Mmm Polojekiti imeneyi inalipo kutsogoloku timati mxii yomwe idayamba kubwera CARE asanafike kweni kwenikuno kwathu, timati chani kodi timakachita maphunziro komwe ko Kayembe uko langondithawaso mxiii limenero lidatithandizaposo mudzi muno, lidatipatsapo chithatha chotengapo maliro, njinga yokanenera matenda kapena kuti njinga yoti wina kudwala addzimkweza panjingapo mwachangu ya mudzi, idalipo ndithu Polojekiti imeneyi nangoiwala Dzina lake mm eyaaa. Nanga olo CARE yi ikugwira ntchito iliposo pulojekiti ina yomwe inabwera kudagwira ntchito yomwe imakuphunzitsani za kadyedwe kabwino ndi zina zotero nthawi yomwe pulojekiti ya CARE imagwira ntchito? Kunabweraso pulojekiti ina? Mmm pulojekiti imeyi ngati inabwera koma ndisanene kuti ngati inabwera koma ndinene kuti ngati ibwere pambuyo pa CARE eyaaa. Kusonyeza kuti panalibeso project ina nthawi yomwe CARE imagwira ntchito? Ayi. Pomwe CARE imagwira ntchito yophunzitsa za kadyedwe mudzi muno? Ayi ngati naiwala chabwino poti ndine munthu ndithu. Owo timafunako titadziwa kuti tingomvetseatsa kuti chasintha kwambiri mudzi muno pankhani ya kadyedwe kabwino ndi chani? Mm mene nili kufotokozera kuti kasintha kadyedwe kabwino mudzi muno aliyese khomo lake lukhala la kadyedwe kabwino chifukwa chama ulamuliro ndi ,ma udindo omwe ali kuchitika mudzi mudzi muno chifukwa maudindo ambiri kale amakhala abambo koma lero lino ngakhale amayi ali mkati. Kadyedwe kabwino mudzi muno kafalikira ndithu. Mukuona ngati chomwe chinabweretsa kusintha kumene kuchitike kumbali yokhudzana kuti panopa anthu mukudziwa za kadyedwe kabwino, aah komaso ana mukuwadyetsa bwino komaso za maudindo pakati pa amayi ndi abambo kuti azimayi mukutha kupatsidwa mwayi otenga nawo gawo, mukuona ngati chomwe chapangitsa, chomwe chabweretsa kusintha kumene kuku ndi chani? Chabweretsa kusintha kumeneku ndi maphunziro omwe mutipatsa inu a CARE, magulu ena amene analipo kale moga mumpingoso amayesetsa ndithu kunena kuti madyedwe abwino ndi ofunika nyumba kuti ana asamanyentchere , mpingoso umayimirirapo kwabasi kuphunzitsa za madyedwe abwin. Oho. Kuti ngakhaleso chalo chathuchi chimayesasa kwabasi kuti madyedwe abwino ndi ofunika pakhomo pa munthu kuti wana asamakhale onyentchera. Mukati chalo mutanthauza a mfumu? Eyaa a mfumu monga a T/A akaonjeza nthawi zambiri amakambako zimenezi kuti madyedwe abwino kudera kuno kukhala ana osanyentchera, ndithu eyaaa . Zikomo. Kumbali ya mudzi munomo ngati za project imeneyiyi za CARE maganizo anu inuyo mukuona kuti mu project imeneyiyi munaikonda? Ngati munaikonda munaikonda bwanji? Inetu , ndifuse nawo pamenepo? Inetu pulojekiti ninayikonda, kuikonda kwa pulojekityi ndi zakuti ikuphunzitsa anthu zambiri pa umoyo wawo. Umoyo wamunthu uli kusintha chifukwa chamaphunziro, pulojekiti yi ya CARE yi nayikonda kwambiri pomwe yabwera ndi mapuhunziro ndithu. Koma poti pulojekiti imathaso mwina simungakonde zose zilipo zomwe project imeyiyi pa zaka zitatu zimenezi pomwe project yi imagwira ntchito zomwe simunazikonde? Mmm pamenepa. Mwina mafusa zisayende choncho? Aaha inetu pulojekiyi nayioknda ndipo ngakhale ili pita kumapeto ilupita popeza zinthu zimakhalira nthawi ahh zimadikira ndithu yochokera koma yochoka koma mwina zambiri anali isanapitase zilimbikitso zoti munthu alimbikire koti njii, koma ili wuchoka ulimbitsowo mabanja ndi mudzi ulipo koma tidikonda ngakhale ili pita ahha ipite koma poti sinanga ndimene zimakhalira koma ineyo daikonda. Koma ndizambiri zomwe zoyenera kuchitik pa moyo wanga, kusintha kwa moyo wanga, pa banga panga ngakhaleso mudzi muno. Ilipo koma sinazione kuti polojekiyi yabweretsa zina zina zosafunika koma kwa ngodandaula kuti ilu pita zambiri monga zitsime mdera lathu lino zosakwanira , zosakwanira zitsime eyaaa , komaso tikhoza kunena kuti timafuna school zakwacha zitakwanira ponse ponse kuti bodza mudzi mwathu muno mudachuluka mbuli azimayi nde amachita manyazi kumawoloka kumapita kokawale amachita manyazi azimayi amanena kuti koma itakhala pamudzi pathu pompano titha kumapita, koma ndiye poti ilu pita kaya mutithandize bwanji ana wanga poti pulojekiti ilupita koma nafuna school yakwacha itakhalapo mudzi mwathu muno. Okulu okulu omachita manyazi kumapita kokawale amachita manyazi chifukwa kalipo kantunda kuchoka mudzi muno ndiye okulu okulu okulu omachita manyazi, koma pulojekiti imeneyi ndi yofunika kowopsya ngakhale ilu tilawira koma zodandaula zathu ndi zimenezi, zitsime sizokwanira ayi chifukwa titha kunena kuti komwe kumachoka bamboo lufeyo kumtunda uko kulibe chitsime chimodzi chomwe cha njigo omalimbirana ndithu pen amachoka kumeneko nthawi yadzuwayi kumadzamwa kuno , kumakamwa kustidya kutsidyakoso ndi chochita kukola palibepo njingo. Njigo mudera lathu lino titha kuweranga kuti njigo uli pano pakwathu ndekuti pokampira mijigo yake ndi iwiri kuzungulira dera linolo, ndithuditu mayi wanga. Mmha ndakunvetsetsani, ndithu , mwanena kuti madzi ndi amene amavuta, njigo ndiyocheap komaso nkhani ya school ya kwacha mdera munomo anthu amafuna ataphunzira koma kulibe school ya kwacha , ndithu, mwina kapena kuliso mavuto ena kumbali yoti maunakakonda kuti project imeneyiyi ikanakhala yapanga mudzi muno mongowonjezera? Eeh pulojekiti imeneyi mudzi mwathu muno , mene nununerera monga school ya kwachayo kapena school ya tiwana kapena kutikonzerako mlatho, bodza kwathu kuno kulibe pulojekiti yomwe imabwera ndi anthu ena kudzakonza mulatho, madzi amathyola pa dziko apa thyoo ndekuti wana school aleka, waleka ana kupita ku school, komaso cehni cheni nufuna, kunoko mutatulako alangizi angapo agulu limeneli chifukwa modziyu aliwutangwanika dera lukula, dera lumukulira nyamatayu eyaa komaso mutatiyikirako mlangizi wina kaya wachikazi kaya ndani kuti adzikhala wugwirizana kuthamanga thamanga, palibe kanthu mulawira koma paj suja amasiyako tiwana. Inuyo project imeyi pa zaka zitatu zomwe yakhala ikugwira ntchito mu dera muno ndi chani chomwe mwapindula pa moyo wanu wa tsiku ndi tsiku? Ngati munthu? Ineyo pa pulojekiti imeyi moyo mwanga ngati munthu zambiri, ngati pa ulimi, naphunziraso kwambiri kulima monga tikatyi kulima limalima chimanga, soya . sawa, fodya ndipo tidaleka mpa nthawi madala athu mkanthawi tidakaleka tidaona kuti songamanyamule zinkhuni zikulu zikulu kuma zika zigafa. Ndiye tapindulako kuti pa uliwo matyiphunzitsa kuti tidzibyala chimanga chimodzi chimodz. Ndiye kuti sawa uku ndi uku monga soya uku ndi uku ndiye zimenezi zandipindulira zedi pamoyo wanga, chifukwa ndimapeza zinthu zambiri zedi pamoyo wanga. Kungoti nthawi yangochepa nakati katiyeni mukaone pomwe nabyala soya, kuchokera kumaphunziro anu mene munatiphunzitsira. Nde moyo wanga upita kapita ndimene munatiphunzitsira, pa banja panga papita pasintha, ndilibe ana. Oho . Ndiyeno nanga kumbali ya mudzi munomo mwaona kusintha komwe project iyi yabweretsa ku moyo wa anthu amudzi muno kumbali ya kadyedwe? Ngakhaleso kumbali ya maudindo ndi kadyedwe? Oho kusintha kulipo monga ndanena kale zasintha ndithu, kale amangopanga ndi abambo maudindo mwina amayi timapondelezedwa koma lero kuli ma udindo yankhani monga ndanena kale VA yamuno tsogoleri wake ndi amayi.
0
30
./data/chichewa-dataset\audio\segment_160.wav
30
60
./data/chichewa-dataset\audio\segment_161.wav
60
90
./data/chichewa-dataset\audio\segment_162.wav
90
120
./data/chichewa-dataset\audio\segment_163.wav
120
150
./data/chichewa-dataset\audio\segment_164.wav
150
180
./data/chichewa-dataset\audio\segment_165.wav
180
210
./data/chichewa-dataset\audio\segment_166.wav
210
240
./data/chichewa-dataset\audio\segment_167.wav
240
270
./data/chichewa-dataset\audio\segment_168.wav
270
300
./data/chichewa-dataset\audio\segment_169.wav
300
330
./data/chichewa-dataset\audio\segment_170.wav
330
360
./data/chichewa-dataset\audio\segment_171.wav
360
390
./data/chichewa-dataset\audio\segment_172.wav
390
420
./data/chichewa-dataset\audio\segment_173.wav
420
450
./data/chichewa-dataset\audio\segment_174.wav
450
480
./data/chichewa-dataset\audio\segment_175.wav
480
510
./data/chichewa-dataset\audio\segment_176.wav
510
540
./data/chichewa-dataset\audio\segment_177.wav
540
570
./data/chichewa-dataset\audio\segment_178.wav
570
600
./data/chichewa-dataset\audio\segment_179.wav
600
630
./data/chichewa-dataset\audio\segment_180.wav
630
660
./data/chichewa-dataset\audio\segment_181.wav
660
690
./data/chichewa-dataset\audio\segment_182.wav
690
720
./data/chichewa-dataset\audio\segment_183.wav
720
750
./data/chichewa-dataset\audio\segment_184.wav
750
780
./data/chichewa-dataset\audio\segment_185.wav
780
810
./data/chichewa-dataset\audio\segment_186.wav
810
840
./data/chichewa-dataset\audio\segment_187.wav
840
870
./data/chichewa-dataset\audio\segment_188.wav
870
900
./data/chichewa-dataset\audio\segment_189.wav
900
930
./data/chichewa-dataset\audio\segment_190.wav
930
960
./data/chichewa-dataset\audio\segment_191.wav
960
990
./data/chichewa-dataset\audio\segment_192.wav
990
1,020
./data/chichewa-dataset\audio\segment_193.wav
1,020
1,050
./data/chichewa-dataset\audio\segment_194.wav
1,050
1,080
./data/chichewa-dataset\audio\segment_195.wav
1,080
1,110
./data/chichewa-dataset\audio\segment_196.wav
1,110
1,140
./data/chichewa-dataset\audio\segment_197.wav
1,140
1,170
./data/chichewa-dataset\audio\segment_198.wav
1,170
1,200
./data/chichewa-dataset\audio\segment_199.wav
1,200
1,230
./data/chichewa-dataset\audio\segment_200.wav
1,230
1,260