sent_id
stringlengths 3
7
⌀ | english
stringlengths 3
1.06k
| chichewa
stringlengths 4
3.03k
| topic
stringclasses 8
values | source
stringclasses 17
values |
---|---|---|---|---|
en13609 | Have you had any trouble conceiving?
| Munali ndi vuto liilonse potenga mimba? | Medical | Book of medical terms |
en13610 | Was the child born premature or late?
| Mwana anabadwa matsiku asanakwane
kapena anabadwa atapitilira masiku? | Medical | Book of medical terms |
en13611 | Did you give birth naturally or C-section?
| Munachira bwino bwino kapena
munabelekera operashoni? | Medical | Book of medical terms |
en13612 | Were you sick during the pregnancy?
| Mumadwala muli ndi mimba? | Medical | Book of medical terms |
en13613 | What was the weight of the baby?
| Mwana anabadwa ndi sikero yanji? | Medical | Book of medical terms |
en13614 | Did you breast feed? Are you breastfeeding?
| Mumayamwisa? Mukuyamwisa? | Medical | Book of medical terms |
en13615 | Does the child have problems with breastfeeding?
| Mwanayu amakhala ndi vuto lililonse poyamwa? | Medical | Book of medical terms |
en13616 | Has the child had any vaccinations?
| Mwanayu analandilapo katemera aliyense? | Medical | Book of medical terms |
en13617 | Is the child breathing properly?
| Mwanayu akumapuma bwinobwino? | Medical | Book of medical terms |
en13618 | Have you noticed anything abnormal
about the child?
| Mwawona china chilichonse chodabwitsa pa
mwanayu? | Medical | Book of medical terms |
en13619 | Does the child stutter a lot?
| Mwanayu ali ndi chibwibwi? | Medical | Book of medical terms |
en13620 | Have you noticed any change in behavior of
the child?
| Mwawonako kusintha kwina kulikonse kwa
chikhalidwe cha mwanayu? | Medical | Book of medical terms |
en13621 | Has the child started eating food or is
he/she still drinking breastmilk?
| Mwanayu wayamba kudya chakudya
china kapena akuyamwabe bere? | Medical | Book of medical terms |
en13622 | What food are you feeding the child?
| Mumamudyetsa chakudya chanji? | Medical | Book of medical terms |
en13623 | Hard or soft foods?
| Zokudya zolimba kapena zofewa? | Medical | Book of medical terms |
en13624 | Is the baby crying more than usual?
| Mwanayu akumalira mopyolera
m’mene amalilira kapena akulira
chimodzimodzi? | Medical | Book of medical terms |
en13625 | Has the child started crawling?
| Mwanayu wayamba kukwawa? | Medical | Book of medical terms |
en13626 | Has the child started walking?
| Mwanayu wayamba kuyenda? | Medical | Book of medical terms |
en13627 | Has the child started speaking?
| Mwanayu wayamba kulankhula? | Medical | Book of medical terms |
en13628 | Is the child able to stand on his/her
own?
| Mwanayu akumatha kuyima pa
yekha? | Medical | Book of medical terms |
en13629 | Is the child able to interact properly
with his/her friends?
| Mwanayu akumatha kusewera bwino
bwino ndi anzake? | Medical | Book of medical terms |
en13630 | How does the urine of the child look?
| Mkodzo wa mwana umawoneka
bwanji? | Medical | Book of medical terms |
en13631 | How does the stool of the child look?
| Chimbuzi cha mwana chimaoneka
bwanji? | Medical | Book of medical terms |
en13632 | Have you ever had an abortion? Why?
| Munayambapo mwatchotsapo
pakati? Chifukwa chani? | Medical | Book of medical terms |
en13633 | Where did you get your abortion?
| Munachotsera kuti mimba yanu? | Medical | Book of medical terms |
en13634 | When did you notice yellowing of the
skin on the child ?
| Munawona kusintha kwa khungu la
mwanayu kubwera chikaso liti? | Medical | Book of medical terms |
en13635 | When did you notice yellowing of the
eyes on the child ?
| Munawona kusintha kwa maso a
mwanayu ali ndi chikaso liti? | Medical | Book of medical terms |
en13636 | Do you feel pressure in your eyes?
| Mumamva kulemedwa mmaso? | Medical | Book of medical terms |
en13637 | Do you feel pain when blinking or
moving your eyes?
| Mumamva kupweteka mukamaphetira
kapena mukamayendetsa maso? | Medical | Book of medical terms |
en13638 | Do you feel like you have sand or
something else in your eye?
| Mumamva ngati muli ndi mchenga
kapena zinthu zina maso mwanu? | Medical | Book of medical terms |
en13639 | Have you noticed your eye twitching?
| Mumamva maso anu akuphetira
kapena kusinzina mosadziwika bwino? | Medical | Book of medical terms |
en13640 | Are you able to see colors well?
| Mumawona mitundu osiyanasiyana
bwino bwino? | Medical | Book of medical terms |
en13641 | Do your eyes feel dry or moist?
| Mumamva maso anu kukhala owuma
kapena onyowa? | Medical | Book of medical terms |
en13642 | Do you have problems closing your
eyes?
| Mumavutika kutseka maso anu? | Medical | Book of medical terms |
en13643 | Are you having difficulty hearing? | Muli ndi vuto lakumva? | Medical | Book of medical terms |
en13644 | Do you hear ringing in your ears? | Mumamva ma belo mmakutu? | Medical | Book of medical terms |
en13645 | Is there any discharge coming out from your ears? | Makutu mwanu mukumatuluka mafinya? | Medical | Book of medical terms |
en13646 | Have you noticed a buildup of earwax? | Mwawonako kuchuluka kwa phula makutu mwanu? | Medical | Book of medical terms |
en13647 | Are your ears sensitive to noises? | Phokoso limakusowetsani mtendere m’makutu mwanu? | Medical | Book of medical terms |
en13648 | Do you use cotton buds? | Mumagwritsa nchito tonje kupukutira makutu? | Medical | Book of medical terms |
en13649 | Do you use earphones? Do you listen to music loudly? | Mumayika zomvetserera nyimbo mmakutu? Mumamvera nyimbozo mokweza? | Medical | Book of medical terms |
en13650 | Do you have hearing aids? | Muli ndi zida zokuthandizani kumva? | Medical | Book of medical terms |
en13651 | Do you see a change when you wear your hearing aids? | Mumawona kusintha mukavala zida zokuthandizani kumva? | Medical | Book of medical terms |
en13652 | Do you play the radio or tv on high volume? | Mumayika wailesi kapena kanema wanu mokweza mukamagwiritsa ntchito? | Medical | Book of medical terms |
en13653 | Do you feel like you lose balance alot? | Mumamva chizungulire pafupi pafupi? | Medical | Book of medical terms |
en13654 | Do you have problems with your sense of smell? | Muli ndi vuto kumva fungo? | Medical | Book of medical terms |
en13655 | Is your nose blocked? | Mphuno zanu ndizotseka? | Medical | Book of medical terms |
en13656 | Have you been sneezing? | Mukuyetsemula? | Medical | Book of medical terms |
en13657 | Does your nose feel like it’s burning? | Mukumva kuwotcha mphuno zanu? | Medical | Book of medical terms |
en13658 | Is there mucus or anything abnormal coming from your nose? | Mphuno mwanu mumatuluka mamina kapena china chilichonse chodabwitsa? | Medical | Book of medical terms |
en13659 | Do you breathe with your mouth? | Mukumapumira mkamwa? | Medical | Book of medical terms |
en13660 | Do you snore? | Mumaliza nkonono? | Medical | Book of medical terms |
en13661 | Are you having difficulty closing your mouth? | Mukuvutika kutseka pakamwa? | Medical | Book of medical terms |
en13662 | Have you noticed any change in your
salivation? (More or less) | Mwawonako kusintha malovu anu
amkamwa? (Kuti akuchuluka kapena
akuchepa? | Medical | Book of medical terms |
en13663 | Are you having any pain when speaking? | Mukumva kupweteka polankhula? | Medical | Book of medical terms |
en13664 | Have you noticed hoarseness in your voice? | Mawo anu akusasa? | Medical | Book of medical terms |
en13665 | Are you having difficulty swallowing? | Mukumavutika kumeza? | Medical | Book of medical terms |
en13666 | Do you feel like there’s something stuck
in your throat/neck?
| Mukumva ngati chinachake chaima
kummero/kukhosi? | Medical | Book of medical terms |
en13667 | Do you have a sore throat? | Muli ndi zilonda ku khosi? | Medical | Book of medical terms |
en13668 | Do you have a mental illness? | Muli ndi vuto la mu ubongo? | Medical | Book of medical terms |
en13669 | Is there anything that bothers you a
a lot?
| Chilipo chimene chimakuvutani
kwambiri? | Medical | Book of medical terms |
en13670 | What makes you anxious/stressed? | Chimakupatsani nkhawa ndi chani? | Medical | Book of medical terms |
en13671 | Have you ever hurt yourself or someone else? | Munazivulazapo kapena kumuvulaza munthu wina? | Medical | Book of medical terms |
en13672 | Is everything okay at home? | Chilichonse chilibwino kunyumba? | Medical | Book of medical terms |
en13673 | Do you feel sick when you don’t drink? | Mumadwala mukakhala kuti simunamwe mowa? | Medical | Book of medical terms |
en13674 | Do you drink alcohol excessively or illegal substance abuse? | Mumamwa mowa kapena mumagwiritsa ntchito mankhwala ozunguza ubongo? | Medical | Book of medical terms |
en13675 | Are you irritable when you don’t drink? | Mumamva kusowa mtendere mukakhala kuti simunamwe? | Medical | Book of medical terms |
en13676 | Do you feel sorry for yourself when you drink? | Mumazimvera chisoni mukamamwa? | Medical | Book of medical terms |
en13677 | Does anyone make you feel that drinking is wrong? | Alipo amene amakuzindikilitsani kuti kuti kumwa mowa ndikoyipa? | Medical | Book of medical terms |
en13678 | Do you see yourself with a future? | Mumaziwona kuti muli ndi tsologo? | Medical | Book of medical terms |
en13679 | Do you think of hurting yourself or others? | Mumaganiza kuti muzivulaze nokha kapena kuwavulaza anthu ena? | Medical | Book of medical terms |
en13680 | Have you ever done something that has risked your life? | Munapangapo china chilichonse chimene chinayikitsa moyo wanu pa chiswe? | Medical | Book of medical terms |
en13681 | Have you ever thought of killing yourself? | Munayambapo mwaganiza zozipha? | Medical | Book of medical terms |
en13682 | Have you noticed yourself being more irritated? | Mumakhala munthu osowa mtendere? | Medical | Book of medical terms |
en13683 | Have you ever been raped or abused? | Munagwiliridwapo? | Medical | Book of medical terms |
en13684 | What do you do to cope with anxiety? | Mumatani kuti musakhale ndi nkhawa? | Medical | Book of medical terms |
en13685 | Do you remember being treated badly as a child? | Mukukumbukira muli mwana ngati mumapangidwa nkhanza? | Medical | Book of medical terms |
en13686 | Do you get violent when you are under the influence of drugs or alcohol? | Mumakhala munthu ovutitsa kwambiri mukakhala kuti mwasuta kapena mwamwa mowa? | Medical | Book of medical terms |
en13687 | Does your drinking cause problems with your work or family? | Kumwa mowa kumakupangitsani kuti muzikhala ndi mavuto ku nchito kapena mbanja lanu? | Medical | Book of medical terms |
en13688 | How do you feel about yourself? | Mumazimva bwanji?/Mumaziwona bwanji? | Medical | Book of medical terms |
en13689 | Do you look down on yourself? | Mumaziyanganira pansi? | Medical | Book of medical terms |
en13690 | Do you feel guilt or shame? | Mumamva kuti mwalakwa kapena mumamva manyazi? | Medical | Book of medical terms |
en13691 | Do you think that you have a purpose? | Mukuganiza kuti muli ndi cholinga? | Medical | Book of medical terms |
en13692 | Do you hear voices that other people can’t hear? | Mumamva mawu ena, amene anthu ena sangamve? | Medical | Book of medical terms |
en13693 | Do you see things that other people can’t see ? | Mumawona zinthu zimene anthu ena sangawone? | Medical | Book of medical terms |
en13694 | What are you worried about? | Mukudandaula chani? | Medical | Book of medical terms |
en13695 | Do you think of killing yourself? | Mumaganiza kuti muziphe nokha? | Medical | Book of medical terms |
en13696 | Do you feel that someone is there
but you can’t see them?
| Mumamva ngati pali munthu koma
simukumuwona? | Medical | Book of medical terms |
en13697 | Are you easily distracted when you are
doing something?
| Mumasokonezeka mukakhala kuti
mukupanga zinthu zina ? | Medical | Book of medical terms |
en13698 | Do you get confused a lot?
| Mumabalalika kwambiri? | Medical | Book of medical terms |
en13699 | What is your mood on most days?
| Mumamva bwanji nthawi zonse? | Medical | Book of medical terms |
en13700 | Do you feel angry, happy, tired?
| Mumakwiya, mumasangalala,
mumakhala otopa? | Medical | Book of medical terms |
en13701 | Have you argued with someone
recently?
| Mwakangana ndi munthu
posachedwapa? | Medical | Book of medical terms |
en13702 | Do you hold grudges?
| Mumasunga mangawa? | Medical | Book of medical terms |
en13703 | Do you think that someone can hear
your thoughts?
| Mumaganiza kuti alipo amene amatha
kukumverani zimene mukulingalira? | Medical | Book of medical terms |
en13704 | Do you think your thoughts are yours?
| Mumaganiza kuti malingaliro amene
mukulingalira ndi anu? | Medical | Book of medical terms |
en13705 | Do you think someone takes away your
thoughts?
| Mumaganiza kuti alipo wina amene
amakuchotserani malingaliro? | Medical | Book of medical terms |
en13706 | Do you think someone controls your
thoughts?
| Mumaganiza kuti alipo wina amene
amalamulira mmalo mwanu? | Medical | Book of medical terms |
en13707 | D o you think that you are a real person?
| Mumaganiza kuti ndinu munthu
weni weni? | Medical | Book of medical terms |
en13708 | Do you think the world is real?
| Mumaganiza kuti dziko lapansi
lilipodi? | Medical | Book of medical terms |